EyooFourth Profile

🎧

Hello there my is Japhet Malola stage name is EyooFourth am an upcoming artist based in Lilongwe I started music in 2018  because of one my family member who likes music and as i was attached to him slowly but surely i fell in love music.

Nyimbo yanga yoyamba kutulutsa anthu ambiri anayikonda pamene ena ankakaikira kunena kuti nyimboyo inali ndi unthenga wa ukulu womwe sizimangwirizana ndi sinkhu wanga, , nyimboyi Title yake inali  #Ndi Ifebe prod by DjBrown

Izi zinandillimbikitsa kulowaso ku studio ndi kutulutsa nyimbo zina ngati  #Iwe,OneDay,Nane& Inap 💥🙏🙌


 

 

Post a Comment

0 Comments